Yohane 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwowa anabadwa kwa Mulungu, osati kudzera m’magazi kapena m’chifuniro cha thupi, kapena chifuniro cha anthu.+ Yohane 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+
13 Iwowa anabadwa kwa Mulungu, osati kudzera m’magazi kapena m’chifuniro cha thupi, kapena chifuniro cha anthu.+
17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+