Salimo 95:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+
7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+