Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova ndi M’busa wanga.+

      Sindidzasowa kanthu.+

  • Salimo 48:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Mulungu uyu ndi Mulungu wathu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+

      Iye adzatitsogolera kufikira imfa yathu.+

  • Salimo 79:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma ife, anthu anu, nkhosa zimene mukuweta,+

      Tidzakuyamikani mpaka kalekale.

      Tidzakutamandani ku mibadwomibadwo.+

  • Salimo 80:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+

      Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+

      Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+

  • Yesaya 40:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+

  • Ezekieli 34:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu ochokera kufumbi. Ine ndine Mulungu wanu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena