Salimo 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya. Salimo 145:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo,+Ndipo adzasimba za zochita zanu zamphamvu.+ Yesaya 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndiponso kuti anthu amene ndinawapanga kuti akhale anga, anene za ulemerero wanga.+
17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.