Salimo 102:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimenezi zalembedwera m’badwo wam’tsogolo.+Ndipo anthu amene adzakhalapo m’tsogolo* adzatamanda Ya.+ Yesaya 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu am’patse Yehova ulemerero,+ ndipo anthu a m’zilumba anene za ulemerero wake.+ Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
18 Zimenezi zalembedwera m’badwo wam’tsogolo.+Ndipo anthu amene adzakhalapo m’tsogolo* adzatamanda Ya.+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+