Salimo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+ Salimo 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya. Yesaya 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndiponso kuti anthu amene ndinawapanga kuti akhale anga, anene za ulemerero wanga.+
31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+
17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.