Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 71:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+

      Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+

      Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+

  • Salimo 78:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mbadwa zawo sitikuzibisira mawu ophiphiritsawa,+

      Ndipo tidzawasimba ngakhale ku mibadwo ya m’tsogolo.+

      Tidzasimba ntchito zotamandika za Yehova ndi mphamvu zake,+

      Komanso zinthu zodabwitsa zimene wachita.+

  • Aroma 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+

  • 1 Akorinto 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena