Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+ Yohane 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu anayankha kuti: “Kodi usana suli ndi maola 12? Munthu akayenda masana+ palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.
34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+
9 Yesu anayankha kuti: “Kodi usana suli ndi maola 12? Munthu akayenda masana+ palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.