Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+

  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+

  • Yesaya 48:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 ine ndinakuuzani zonse kuyambira nthawi imeneyo. Ndinakuuzani zisanachitike,+ kuti musadzanene kuti, ‘Fano langa ndi limene lachita zimenezi, ndipo chifaniziro changa chosema komanso chifaniziro changa chopangidwa ndi chitsulo chosungunula, n’zimene zalamula zimenezi.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena