Maliko 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+
32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+