Oweruza 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo analibe owalanditsa chifukwa mzindawo unali kutali ndi Sidoni+ ndipo sankayenderana ndi anthu a m’madera ena. Komanso, mzindawo unali m’chigwa cha Beti-rehobu.+ Choncho ana a Dani anamanganso mzindawo ndi kuyamba kukhalamo.+ Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
28 Iwo analibe owalanditsa chifukwa mzindawo unali kutali ndi Sidoni+ ndipo sankayenderana ndi anthu a m’madera ena. Komanso, mzindawo unali m’chigwa cha Beti-rehobu.+ Choncho ana a Dani anamanganso mzindawo ndi kuyamba kukhalamo.+
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+