Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 M’masiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri+ inabwera n’kulanda Iyoni,+ Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori,+ Giliyadi,+ ndi Galileya,+ dziko lonse la Nafitali.+ Inatenga anthu a m’madera amenewa n’kupita nawo ku Asuri.+

  • 2 Mafumu 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno mfumu ya Asuri inabwera kudzachita nkhondo ndi dziko lonselo, kenako inazungulira mzinda wa Samariya+ kwa zaka zitatu.

  • 2 Mafumu 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iweyo wamva zimene mafumu a Asuri anachita kumayiko onse amene anawawononga.+ Ndiye kodi iweyo ukuona ngati upulumuka?+

  • Yesaya 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Dzanja langa+ lidzafikira chuma+ cha mitundu ya anthu ngati likupisa m’chisa. Ngati mmene munthu amatengera mazira amene asiyidwa, ine ndidzatenga dziko lonse lapansi. Sipadzakhala aliyense wokupiza mapiko ake kapena wotsegula pakamwa pake, kapenanso wolira ngati mbalame.’”

  • Yesaya 37:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa?+ Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena