Numeri 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+ Deuteronomo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Makiri+ ndinam’patsa Giliyadi.+
40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+