Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”

  • 1 Mbiri 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Baala anabereka Beeraha yemwe Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri inam’tenga kupita naye ku ukapolo. Iye anali mtsogoleri wa Arubeni.

  • 1 Mbiri 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho, Mulungu wa Isiraeli analimbikitsa mtima+ wa Puli+ mfumu ya Asuri,+ ndithu analimbikitsa mtima wa Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri, moti anatenga+ Arubeni, Agadi, ndi hafu ya fuko la Manase n’kuwapititsa ku Hala,+ ku Habori, ku Hara, ndi kumtsinje wa Gozani, ndipo akukhalabe kumeneko mpaka lero.

  • 2 Mbiri 28:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena