2 Mafumu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu ya Asuri inabwera kudzachita nkhondo ndi dziko lonselo, kenako inazungulira mzinda wa Samariya+ kwa zaka zitatu. Yesaya 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “M’tsiku limenelo, pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,*+ pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ Yehova adzameta tsitsi la kumutu ndi tsitsi la m’mapazi, ndipo lezalalo lidzachotseratu ngakhale ndevu.+
5 Ndiyeno mfumu ya Asuri inabwera kudzachita nkhondo ndi dziko lonselo, kenako inazungulira mzinda wa Samariya+ kwa zaka zitatu.
20 “M’tsiku limenelo, pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,*+ pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ Yehova adzameta tsitsi la kumutu ndi tsitsi la m’mapazi, ndipo lezalalo lidzachotseratu ngakhale ndevu.+