2 Mafumu 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.” 2 Mbiri 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse.
7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”
20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse.