Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 M’masiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri+ inabwera n’kulanda Iyoni,+ Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori,+ Giliyadi,+ ndi Galileya,+ dziko lonse la Nafitali.+ Inatenga anthu a m’madera amenewa n’kupita nawo ku Asuri.+

  • 2 Mafumu 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”

  • 1 Mbiri 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho, Mulungu wa Isiraeli analimbikitsa mtima+ wa Puli+ mfumu ya Asuri,+ ndithu analimbikitsa mtima wa Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri, moti anatenga+ Arubeni, Agadi, ndi hafu ya fuko la Manase n’kuwapititsa ku Hala,+ ku Habori, ku Hara, ndi kumtsinje wa Gozani, ndipo akukhalabe kumeneko mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena