1 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a gulu lake lankhondo kuti akamenyane ndi mizinda ya Isiraeli. Iwo anawononga mizinda ya Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka,+ ndi Kinereti yense mpaka dziko lonse la Nafitali.+
20 Choncho Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a gulu lake lankhondo kuti akamenyane ndi mizinda ya Isiraeli. Iwo anawononga mizinda ya Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka,+ ndi Kinereti yense mpaka dziko lonse la Nafitali.+