2 Samueli 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Sheba anadutsa pakati pa mafuko onse a Isiraeli kupita kumzinda wa Abele wa ku Beti-maaka.+ Nawonso Abikiri onse anasonkhana ndi kuyamba kumuthamangitsa.
14 Tsopano Sheba anadutsa pakati pa mafuko onse a Isiraeli kupita kumzinda wa Abele wa ku Beti-maaka.+ Nawonso Abikiri onse anasonkhana ndi kuyamba kumuthamangitsa.