2 Samueli 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Sheba anadutsa mafuko onse a Isiraeli nʼkukafika kumzinda wa Abele wa ku Beti-maaka.+ Nawonso Abikiri onse anasonkhana nʼkuyamba kumutsatira.
14 Tsopano Sheba anadutsa mafuko onse a Isiraeli nʼkukafika kumzinda wa Abele wa ku Beti-maaka.+ Nawonso Abikiri onse anasonkhana nʼkuyamba kumutsatira.