Genesis 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anatenga chuma chawo chonse, ndipo ana awo onse ang’onoang’ono ndi akazi awo anawagwira ndi kupita nawo. Anatenga zonse zimene zinali m’nyumba zawo.+ Yesaya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 popeza mwanayo asanadziwe kuitana+ kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ anthu adzanyamula chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya n’kupita naye pamaso pa mfumu ya Asuri.”+
29 Anatenga chuma chawo chonse, ndipo ana awo onse ang’onoang’ono ndi akazi awo anawagwira ndi kupita nawo. Anatenga zonse zimene zinali m’nyumba zawo.+
4 popeza mwanayo asanadziwe kuitana+ kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ anthu adzanyamula chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya n’kupita naye pamaso pa mfumu ya Asuri.”+