Ekisodo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Pomwepo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Tachitanji pamenepa polola akapolo athu Aisiraeli kuchoka?”+ Yesaya 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko amenewa, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+
5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Pomwepo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Tachitanji pamenepa polola akapolo athu Aisiraeli kuchoka?”+
20 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko amenewa, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+