2 Mafumu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+ 2 Mafumu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 N’zoonadi Yehova, kuti mafumu a Asuri awononga mitundu ndi mayiko awo.+
35 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+