-
2 Mbiri 32:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Tsopano musalole kuti Hezekiya akupusitseni+ kapena kukunyengererani+ chonchi ndipo musamukhulupirire, chifukwa palibe ufumu uliwonse kapena mulungu wa mtundu uliwonse wa anthu amene anatha kupulumutsa anthu akewo m’manja mwanga ndiponso m’manja mwa makolo anga. Ndiye mukuganiza kuti Mulungu wanu angakupulumutseni m’manja mwanga?’”+
-
-
Yobu 15:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Popeza amatambasula dzanja lake motsutsana ndi Mulungu,
Ndipo amayesera kuti akhale wamkulu kuposa Wamphamvuyonse,+
-