2 Mafumu 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mfumuyo yanena kuti, ‘Musalole kuti Hezekiya akunamizeni anthu inu, chifukwa sangathe kukulanditsani m’manja mwanga.+ 2 Mafumu 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
29 Mfumuyo yanena kuti, ‘Musalole kuti Hezekiya akunamizeni anthu inu, chifukwa sangathe kukulanditsani m’manja mwanga.+
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+