Yesaya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukumudalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+