Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+

  • Deuteronomo 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+

      Kuti adani awo angamve molakwa,+

      Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+

      Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+

  • Danieli 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano ngati mwakonzeka kuti mukamva kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamng’ono, zoimbira zosiyanasiyana za zingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zosiyanasiyana zoimbira,+ mugwada n’kuwerama mpaka nkhope zanu pansi ndi kulambira fano lagolide, zili bwino. Koma ngati simulilambira, nthawi yomweyo muponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto. Ndipo ndi mulungu uti amene angakupulumutseni m’manja mwanga?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena