Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+

  • 2 Mbiri 32:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano musalole kuti Hezekiya akupusitseni+ kapena kukunyengererani+ chonchi ndipo musamukhulupirire, chifukwa palibe ufumu uliwonse kapena mulungu wa mtundu uliwonse wa anthu amene anatha kupulumutsa anthu akewo m’manja mwanga ndiponso m’manja mwa makolo anga. Ndiye mukuganiza kuti Mulungu wanu angakupulumutseni m’manja mwanga?’”+

  • Yesaya 36:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndi mulungu uti pakati pa milungu yonse ya mayiko amenewa, amene walanditsa dziko lake m’manja mwanga,+ kuti Yehova athe kulanditsa Yerusalemu m’manja mwanga?”’”+

  • Yesaya 37:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+

      Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+

      Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+

      Ndi Woyera wa Isiraeli!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena