Salimo 115:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musalole kuti mitundu izinena kuti:+“Mulungu wawo ali kuti tsopano?”+ Salimo 140:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, munthu woipa musam’patse zimene mtima wake umafuna.+Musalole kuti chiwembu chawo chitheke chifukwa angadzikweze.+ [Seʹlah.]
8 Inu Yehova, munthu woipa musam’patse zimene mtima wake umafuna.+Musalole kuti chiwembu chawo chitheke chifukwa angadzikweze.+ [Seʹlah.]