Salimo 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Salimo 79:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+ Ife tidzaone ndi maso athu.+ Yoweli 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Ansembe ndi atumiki a Yehova alire m’khonde mwa guwa lansembe+ ndipo anene kuti, ‘Inu Yehova, mverani chisoni anthu anu ndipo musachititse manyazi cholowa chanu+ kuti mitundu ya anthu iwalamulire. Anthu a mitundu ina asanene kuti: “Kodi Mulungu wawo ali kuti?”’+
3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+ Ife tidzaone ndi maso athu.+
17 “Ansembe ndi atumiki a Yehova alire m’khonde mwa guwa lansembe+ ndipo anene kuti, ‘Inu Yehova, mverani chisoni anthu anu ndipo musachititse manyazi cholowa chanu+ kuti mitundu ya anthu iwalamulire. Anthu a mitundu ina asanene kuti: “Kodi Mulungu wawo ali kuti?”’+