Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ponena za moyo wanga, ambiri akuti:“Mulungu sam’pulumutsa ameneyu.”+ [Seʹlah.*] Salimo 79:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+ Ife tidzaone ndi maso athu.+
10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+ Ife tidzaone ndi maso athu.+