Ekisodo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka. Numeri 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukapha anthuwa kamodzi n’kamodzi ngati mukupha munthu mmodzi,+ ndithu mitundu imene yamva za ukulu wanu idzati, Deuteronomo 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+
12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka.
15 Mukapha anthuwa kamodzi n’kamodzi ngati mukupha munthu mmodzi,+ ndithu mitundu imene yamva za ukulu wanu idzati,
27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+