Ekisodo 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+ Salimo 105:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Analola adaniwo kusintha mitima yawo ndi kudana ndi anthu ake,+Anawalola kuchitira atumiki ake zachinyengo.+
33 Choncho Aiguputo anaumiriza anthuwo kuti achoke m’dzikolo mofulumira.+ Iwo anati, “chifukwa tonsefe tikungokhala ngati tafa kale!”+
25 Analola adaniwo kusintha mitima yawo ndi kudana ndi anthu ake,+Anawalola kuchitira atumiki ake zachinyengo.+