Oweruza 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova anatumiza munthu wina, mneneri,+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndine amene ndinakutulutsani mu Iguputo,+ m’nyumba yaukapolo.+ 1 Samueli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+ 1 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+
8 Yehova anatumiza munthu wina, mneneri,+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndine amene ndinakutulutsani mu Iguputo,+ m’nyumba yaukapolo.+
27 Ndiyeno munthu wa Mulungu+ anapita kwa Eli ndi kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinadzisonyeze kunyumba ya kholo lako pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+
6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+