Ekisodo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yehova anamukwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi Aroni Mlevi si m’bale wako?+ Ndikudziwa kuti amatha kulankhula. Ndiponso, iye ali m’njira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+ Ekisodo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.
14 Zitatero, Yehova anamukwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi Aroni Mlevi si m’bale wako?+ Ndikudziwa kuti amatha kulankhula. Ndiponso, iye ali m’njira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+
27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.