Oweruza 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+ Salimo 78:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+ Salimo 136:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yamikani amene anatulutsa Aisiraeli pakati pawo:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+
52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+
11 Yamikani amene anatulutsa Aisiraeli pakati pawo:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+