Oweruza 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu, ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo nʼkukulowetsani mʼdziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Ndinanenanso kuti, ‘Sindidzaphwanya pangano langa ndi inu.+
2 Kenako mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu, ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo nʼkukulowetsani mʼdziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Ndinanenanso kuti, ‘Sindidzaphwanya pangano langa ndi inu.+