1 Mbiri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova, ndiye anapanga kumwamba.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
26 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova, ndiye anapanga kumwamba.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+