2 Mafumu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+ Yeremiya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+
13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+
23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+