Yesaya 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko wachotsedwa kuti asakhalenso mzinda, ndipo wakhala bwinja, wakhala mulu wa zinthu zogumukagumuka.+ Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.
17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko wachotsedwa kuti asakhalenso mzinda, ndipo wakhala bwinja, wakhala mulu wa zinthu zogumukagumuka.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.