1 Mbiri 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya. Yeremiya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+ Amosi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’
5 Pamene Asiriya a ku Damasiko anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba,+ Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.
23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’