2 Mafumu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha. Yesaya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango. Amosi 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova akufunsa kuti, ‘Inu ana a Isiraeli, kodi simuli ngati ana a Akusi kwa ine? Kodi si ndine amene ndinatulutsa Aisiraeli m’dziko la Iguputo,+ amenenso ndinatulutsa Afilisiti+ ku Kerete komanso Asiriya ku Kiri?’+
9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha.
6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango.
7 “Yehova akufunsa kuti, ‘Inu ana a Isiraeli, kodi simuli ngati ana a Akusi kwa ine? Kodi si ndine amene ndinatulutsa Aisiraeli m’dziko la Iguputo,+ amenenso ndinatulutsa Afilisiti+ ku Kerete komanso Asiriya ku Kiri?’+