Ekisodo 12:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo. Hoseya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+ Amosi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+
51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo.
13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+
10 Koma ine ndinatulutsa anthu inu m’dziko la Iguputo+ ndi kukuyendetsani m’chipululu zaka 40+ kuti mukatenge dziko la Aamori.+