2 Mafumu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha. Yesaya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango. Amosi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’
9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha.
6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango.
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’