Amosi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’