Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+ Yesaya 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko wachotsedwa kuti asakhalenso mzinda, ndipo wakhala bwinja, wakhala mulu wa zinthu zogumukagumuka.+
8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+
17 Uwu ndi uthenga wokhudza Damasiko:+ “Taonani! Damasiko wachotsedwa kuti asakhalenso mzinda, ndipo wakhala bwinja, wakhala mulu wa zinthu zogumukagumuka.+