Genesis 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+
37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+