Rute 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kapitawoyo anayankha kuti: “Mtsikana ameneyu ndi Mmowabu+ amene anabwera limodzi ndi Naomi kuchokera ku Mowabu.+ 1 Mbiri 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagonjetsa Mowabu,+ moti Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+
6 Kapitawoyo anayankha kuti: “Mtsikana ameneyu ndi Mmowabu+ amene anabwera limodzi ndi Naomi kuchokera ku Mowabu.+
2 Kenako anagonjetsa Mowabu,+ moti Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo anali kukhoma msonkho kwa iye.+