Rute 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako, anawo anakwatira akazi achimowabu.+ Wina dzina lake anali Olipa, wina anali Rute.+ Ndipo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.
4 Kenako, anawo anakwatira akazi achimowabu.+ Wina dzina lake anali Olipa, wina anali Rute.+ Ndipo anakhalabe kumeneko zaka pafupifupi 10.