Ezekieli 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndikutambasula dzanja langa kuti ndilange Afilisiti,+ ndipo ndidzapha Akereti+ ndi kuwononga anthu onse okhala m’mbali mwa nyanja.+ Amosi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’
16 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndikutambasula dzanja langa kuti ndilange Afilisiti,+ ndipo ndidzapha Akereti+ ndi kuwononga anthu onse okhala m’mbali mwa nyanja.+
8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’